| 1. Padziko tikhala zovuta mzambiriWe are living in a world of difficulties
 Komatu (komatu) tidziwe (tidziwe) ambuye sangatitaye
 But know that the Lord will not forsake us
 Ngakhale satana ali padzikol
 Though satan dwells in this world
 Tiyeni (tiyeni) tilimbe (tilimbe ) osabwerera mmbuyo
 Let us all stand strong, no
               turning, no turning back
 | 2. Tipemphe Ambuye atitsogolereWe ask you our Lord to lead us on the way
 ulendo (ulendo ) wopita (wopita) kumwamba kuli atate
 on the way going to that home
 komweko kulibe matenda kulira
 Where there are no diseases, nor weeping
 zobvuta (zovuta) umphawi (uimphawi ) imfayo singafikeko
 Problems, poverty, even death is
               not there
 |