| Download this file to print out bookmarks
               with the Lord's Prayer on each side - one side in English and
               the other in Chichewa.     | Pemphero la Ambuye Atate wathu wa kumwamba,dzina lanu liyeretsedwe,
 ufumu wanu udze,
 kufuna kwanu kuchitidwe,
 monga kumwamba chomwecho pansi pano.
 Mutipatse ife lero chakudya chathu chalero,ndipo mutikhululukire ife machimo athu,
 monga ifenso tiwakhululukira otichimwira,
 musatitengere ife kokatiyesa,
 koma mutipulumutse ife kwa woipayo.
 
 Chifukwa wanu uli ufumu ndi mphamvu ndi
 ulemerero wa nthawi zonse.
 Amen.
 |